Ekisodo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anasungadi chakudyacho mpaka m’mawa monga momwe Mose anawalamulira, ndipo sichinanunkhe kapena kuchita mphutsi.+
24 Choncho anasungadi chakudyacho mpaka m’mawa monga momwe Mose anawalamulira, ndipo sichinanunkhe kapena kuchita mphutsi.+