Ekisodo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nthawi yomweyo Mose anamvera zimene apongozi ake anamuuza ndipo anachita zonse zimene ananena.+