Ekisodo 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati dzuwa linali litatuluka, amene wamuphayo ali ndi mlandu wa magazi.) “Wakuba azilipira ndithu. Ngati alibe kalikonse, pamenepo azigulitsidwa kuti alipire zinthu zimene anabazo.+
3 Ngati dzuwa linali litatuluka, amene wamuphayo ali ndi mlandu wa magazi.) “Wakuba azilipira ndithu. Ngati alibe kalikonse, pamenepo azigulitsidwa kuti alipire zinthu zimene anabazo.+