-
Ekisodo 22:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 “Munthu akapatsa mnzake bulu, ng’ombe, nkhosa kapena chiweto chilichonse kuti amusungire, ndipo chafa, chalumala kapena chabedwa popanda woona zimene zachitika,
-