Ekisodo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Mnzako ukamulanda chovala chake monga chikole,+ uzim’bwezera dzuwa likamalowa. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2017, tsa. 9