Ekisodo 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mose yekha ayandikire kwa Yehova, koma enawo asayandikire. Anthu ena onse asakwere m’phiri.”+