Ekisodo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anatuma anyamata a Isiraeli ndipo anyamatawo anapereka nsembe zopsereza komanso anapereka ng’ombe kuti zikhale nsembe zachiyanjano+ kwa Yehova.
5 Kenako anatuma anyamata a Isiraeli ndipo anyamatawo anapereka nsembe zopsereza komanso anapereka ng’ombe kuti zikhale nsembe zachiyanjano+ kwa Yehova.