Ekisodo 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu sanawononge atsogoleri amenewo a ana a Isiraeli,+ koma iwo anaona masomphenya a Mulungu woona+ ndipo anadya ndi kumwa.+
11 Mulungu sanawononge atsogoleri amenewo a ana a Isiraeli,+ koma iwo anaona masomphenya a Mulungu woona+ ndipo anadya ndi kumwa.+