Ekisodo 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ulandire ndalama zasiliva zophimbira machimo kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wa pachihema chokumanako+ monga dipo la miyoyo yanu, pophimba machimo anu, kuti Yehova akumbukire ana a Isiraeli.”
16 Choncho ulandire ndalama zasiliva zophimbira machimo kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wa pachihema chokumanako+ monga dipo la miyoyo yanu, pophimba machimo anu, kuti Yehova akumbukire ana a Isiraeli.”