Ekisodo 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Polowa m’chihema chokumanako, kapena popita kukatumikira paguwa lansembe, kukapereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto,+ azisamba kuti asafe. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:20 Nsanja ya Olonda,7/1/1996, tsa. 9
20 Polowa m’chihema chokumanako, kapena popita kukatumikira paguwa lansembe, kukapereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto,+ azisamba kuti asafe.