Ekisodo 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Azisamba m’manja ndi mapazi awo kuti asafe.+ Limeneli ndi lamulo kwa iwo mpaka kalekale, likhale lamulo kwa Aroni ndi ana ake ku mibadwo yawo yonse.”+
21 Azisamba m’manja ndi mapazi awo kuti asafe.+ Limeneli ndi lamulo kwa iwo mpaka kalekale, likhale lamulo kwa Aroni ndi ana ake ku mibadwo yawo yonse.”+