Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzoze Aroni+ ndi ana ake,+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+