Ekisodo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova analankhulanso ndi Mose kuti: “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Inu ndinu anthu ouma khosi.+ Ndingathe kulowa pakati panu ndi kukufafanizani m’kamphindi.+ Chotero, vulani zodzikongoletsera, pakuti ndikufuna kuona choti ndikuchiteni.’”+
5 Ndiyeno Yehova analankhulanso ndi Mose kuti: “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Inu ndinu anthu ouma khosi.+ Ndingathe kulowa pakati panu ndi kukufafanizani m’kamphindi.+ Chotero, vulani zodzikongoletsera, pakuti ndikufuna kuona choti ndikuchiteni.’”+