Ekisodo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Mose akatuluka mumsasawo kupita kuchihema, anthu onse anali kuimirira.+ Aliyense anali kuimirira pakhomo la hema wake, n’kumayang’anitsitsa Mose kufikira atalowa m’chihema.
8 Ndiyeno Mose akatuluka mumsasawo kupita kuchihema, anthu onse anali kuimirira.+ Aliyense anali kuimirira pakhomo la hema wake, n’kumayang’anitsitsa Mose kufikira atalowa m’chihema.