Ekisodo 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero Yehova anatinso kwa Mose: “Ndidzachita izinso zimene wanena,+ chifukwa ndakukomera mtima ndipo ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe.”
17 Chotero Yehova anatinso kwa Mose: “Ndidzachita izinso zimene wanena,+ chifukwa ndakukomera mtima ndipo ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe.”