-
Ekisodo 33:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho pamene ulemerero wanga ukudutsa pafupi ndi iwe, ndidzakuika kuphanga la thanthwelo, ndipo ndidzakuphimba ndi dzanja langa mpaka nditadutsa.
-