-
Ekisodo 34:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chotero Mose anasemadi miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija, ndipo anadzuka m’mamawa ndi kukwera m’phiri la Sinai, atanyamula miyala iwiriyo m’manja mwake, monga momwe Yehova anam’lamulira.
-