Ekisodo 36:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno anakuta mafelemuwo ndi golide, ndipo anapanga mphete zake zagolide zolowetsamo mipiringidzo. Mipiringidzoyo anaikuta ndi golide.+
34 Ndiyeno anakuta mafelemuwo ndi golide, ndipo anapanga mphete zake zagolide zolowetsamo mipiringidzo. Mipiringidzoyo anaikuta ndi golide.+