Levitiko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.
5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.