Levitiko 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo ana a Aroni, ansembe, aziika moto paguwa lansembelo+ ndi kuyalapo nkhuni.+