Levitiko 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno azitsuka matumbo+ ndi ziboda+ ndi madzi. Kenako wansembe azitenga nyama yonseyo ndi kuitentha+ paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yopsereza, nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+
13 Ndiyeno azitsuka matumbo+ ndi ziboda+ ndi madzi. Kenako wansembe azitenga nyama yonseyo ndi kuitentha+ paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yopsereza, nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+