Levitiko 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Wansembe azibweretsa mbalameyo paguwa lansembe ndi kudula*+ mutu wake. Akatero aziitentha paguwa lansembe, koma magazi ake aziwakhetsera pansi pambali pa guwa lansembelo.
15 Wansembe azibweretsa mbalameyo paguwa lansembe ndi kudula*+ mutu wake. Akatero aziitentha paguwa lansembe, koma magazi ake aziwakhetsera pansi pambali pa guwa lansembelo.