Levitiko 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muzithira mafuta ndi kuika lubani pansembeyo. Imeneyi ndi nsembe yambewu.+