Levitiko 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Azichotsanso impso ziwiri ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta+ a pachiwindi, aziwachotsa pamodzi ndi impsozo.
10 Azichotsanso impso ziwiri ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta+ a pachiwindi, aziwachotsa pamodzi ndi impsozo.