Levitiko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyama ya nsembe zachiyanjano zoperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge iliyonse ya nyamayo kufika m’mawa.+
15 Nyama ya nsembe zachiyanjano zoperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge iliyonse ya nyamayo kufika m’mawa.+