Levitiko 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Munthu amene wadya nyama ya nsembe yachiyanjano, imene ndi ya Yehova, pamene munthuyo ali wodetsedwa, aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
20 “‘Munthu amene wadya nyama ya nsembe yachiyanjano, imene ndi ya Yehova, pamene munthuyo ali wodetsedwa, aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+