Levitiko 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti aliyense wodya mafuta a nyama imene waipereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, munthu ameneyo aziphedwa+ kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.
25 Pakuti aliyense wodya mafuta a nyama imene waipereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, munthu ameneyo aziphedwa+ kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.