Levitiko 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo wansembe+ aziona nthendayo, ndipo azisunga chinthucho kwachokha+ masiku 7.