-
Levitiko 14:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Ndiyeno wansembe alamule kuti apale mkati mwa nyumba yonseyo, ndi kutaya dothi lomangira limene agumulalo kunja kwa mzinda, kumalo odetsedwa.
-