Levitiko 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Aliyense wa inu aziopa mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, ptsa. 4-5, 8
3 “‘Aliyense wa inu aziopa mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.