Levitiko 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo munthu wodya nyamayo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho,+ chifukwa waipitsa chinthu chopatulika cha Yehova. Munthu wotero aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
8 Ndipo munthu wodya nyamayo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho,+ chifukwa waipitsa chinthu chopatulika cha Yehova. Munthu wotero aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.