Levitiko 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Malamulo angawa muziwasunga: Musakweranitse ziweto zanu zosiyana. Pobzala mbewu m’munda mwanu musasakanize mitundu iwiri yosiyana.+ Ndipo musamavale chovala cha ulusi wa mitundu iwiri yosakaniza.*+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, tsa. 6
19 “‘Malamulo angawa muziwasunga: Musakweranitse ziweto zanu zosiyana. Pobzala mbewu m’munda mwanu musasakanize mitundu iwiri yosiyana.+ Ndipo musamavale chovala cha ulusi wa mitundu iwiri yosakaniza.*+