-
Levitiko 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 “‘Mwamuna akagona ndi mtsikana wantchito wofunsiridwa ndi mwamuna wina, ndipo mkaziyo sanawomboledwe m’njira ina iliyonse kapena kupatsidwa ufulu, pazikhala chilango. Iwo asaphedwe chifukwa mkaziyo anali asanakhale mfulu.
-