Levitiko 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno wansembe aziphimba tchimo limene munthuyo wachita. Azitero popereka kwa Yehova nkhosa yamphongo ya nsembe ya kupalamula ija. Pamenepo munthuyo azikhululukidwa tchimo lakelo.+
22 Ndiyeno wansembe aziphimba tchimo limene munthuyo wachita. Azitero popereka kwa Yehova nkhosa yamphongo ya nsembe ya kupalamula ija. Pamenepo munthuyo azikhululukidwa tchimo lakelo.+