-
Levitiko 19:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 “‘Mukafika m’dziko limene mukupita n’kubzala mtengo uliwonse wa zipatso, muziuona ngati wosadulidwa, ndipo zipatso zake zizikhala zodetsedwa kwa inu. Muziona mtengowo kukhala wosadulidwa kwa zaka zitatu ndipo musamadye zipatso zake.
-