Levitiko 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo.+ Musamachite chinyengo poyeza utali wa chinthu, kulemera kwa chinthu+ kapena poyeza zinthu zamadzi. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:35 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, tsa. 10
35 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo.+ Musamachite chinyengo poyeza utali wa chinthu, kulemera kwa chinthu+ kapena poyeza zinthu zamadzi.