Levitiko 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Muzisunga malangizo anga onse ndi zigamulo zanga zonse, ndipo muzizitsatira.+ Ine ndine Yehova.’”