Levitiko 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzisunga malamulo anga.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani monga anthu oyera.+