Levitiko 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.
14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.