Levitiko 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Mwamuna akagona ndi mkazi amene ali pa nyengo ya kusamba, onse awiri sanalemekeze magazi ake.+ Choncho onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:18 Nsanja ya Olonda,6/1/1989, tsa. 14
18 “‘Mwamuna akagona ndi mkazi amene ali pa nyengo ya kusamba, onse awiri sanalemekeze magazi ake.+ Choncho onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.