Levitiko 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo mwamuna wogona ndi mkazi wa m’bale wa bambo ake, wavula m’bale wa bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziyankha mlandu wa tchimo lawolo. Ayenera kufa kuti asabereke ana.+
20 Ndipo mwamuna wogona ndi mkazi wa m’bale wa bambo ake, wavula m’bale wa bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziyankha mlandu wa tchimo lawolo. Ayenera kufa kuti asabereke ana.+