Levitiko 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukhale oyera kwa ine,+ chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukupatulani kwa anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:26 Nsanja ya Olonda,11/1/1987, tsa. 11
26 Mukhale oyera kwa ine,+ chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukupatulani kwa anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+