Levitiko 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.
14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.