Levitiko 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Musaipitse dzina langa loyera,+ m’malomwake muzindiona kukhala wopatulika pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani kuti mukhale oyera.+
32 Musaipitse dzina langa loyera,+ m’malomwake muzindiona kukhala wopatulika pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani kuti mukhale oyera.+