Levitiko 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mum’tulutsire kunja kwa msasa.+ Onse amene anamumva aike manja awo+ pamutu pake ndipo khamu lonse lim’ponye miyala.+
14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mum’tulutsire kunja kwa msasa.+ Onse amene anamumva aike manja awo+ pamutu pake ndipo khamu lonse lim’ponye miyala.+