-
Levitiko 25:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 “‘Muziwerenga masabata 7 azaka, zaka 7 kuchulukitsa maulendo 7. Masiku onse a masabata 7 azaka azikwana zaka 49.
-