Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, ptsa. 8-9 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148 Mtendere Weniweni, ptsa. 99-100
10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
25:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, ptsa. 8-9 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148 Mtendere Weniweni, ptsa. 99-100