Levitiko 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chaka cha 50 ndi Chaka cha Ufulu kwa inu.+ Musalime minda yanu kapena kukolola mbewu zomera zokha, kapenanso kukolola mphesa za m’mitengo yosadulirayo.+
11 Chaka cha 50 ndi Chaka cha Ufulu kwa inu.+ Musalime minda yanu kapena kukolola mbewu zomera zokha, kapenanso kukolola mphesa za m’mitengo yosadulirayo.+