Levitiko 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Mwina munganene kuti: “Popeza sitidzalima minda yathu ndi kukolola mbewu zathu, tidzadya chiyani m’chaka cha 7?”+
20 “‘Mwina munganene kuti: “Popeza sitidzalima minda yathu ndi kukolola mbewu zathu, tidzadya chiyani m’chaka cha 7?”+