Levitiko 25:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Musam’kongoze ndalama kuti adzabweze chiwongoladzanja,+ ndipo musakongoze chakudya chanu mwa kuchititsa katapira. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:37 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 24
37 Musam’kongoze ndalama kuti adzabweze chiwongoladzanja,+ ndipo musakongoze chakudya chanu mwa kuchititsa katapira.